
A Usi ayendera ntchito yogawa phala
Dzulo laliwisili, wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino, a Michael Usi, adali m’boma la Dowa komwe adakayendera ntchito yopereka phala kwa ophunzira a pa sukulu ya pulaimale ya Changalu. Ntchito yogawa phalayi imagwiridwa ndi bungwe… ...