ADMARC yakweza mtengo ogulira chimanga
Ngati njira imodzi yokopera alimi kuti akagulitse chimanga chawo ku bungwe logula ndikugulitsa mbewu la ADMARC, bungweli lakweza mtengo omwe likugulira chimanga. Malingana ndi chi kalata chomwe tawona, bungweli lidzigula chimanga pa mtengo wa K700… ...