
Otsutsa akanalimbikitsa ulimi wa fodya osati ma demo bwezi tili patali – Chakwera
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati ululu wa kukwera kwa mitengo ya zinthu mdziko lino bwezi uli owonjeza pakadapanda alimi a fodya pomwe wati otsutsa akanalimbikitsa ulimi wafodya osati ziwonetselo bwezi Malawi atapita patali.… ...