
Musaganize kuti mungatembenuze zinthu mu miyezi iwiri – Chimwendo Banda
Mlembi wamkulu wachipani cha Malawi Congress (MCP) Richard Chimwendo Banda yemwenso ndi mkulu wa zokambilana mnyumba ya malamulo wati kukhala kovuta kuti andale ena athe kutembenuza zinthu mu miyezi yochepa pamene chisankho chayandikira ngati zakanika… ...