Chief Juma

Mfumu imangiliridwa ku mtengo

Tsoka likalimba amakulumadi ndi galu wako yemwe, ku m'mawa-ku adzukulu am'mudzi wa Maula, m'boma la Mchinji, T/A Ndawambe, amangilira kumtengo mfumu yawo a Juma kaamba koti asokoneza ndalama zachipepeso zomwe zimayenera kupita kwa anamfedwa. Malingana… ...