Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1
Kuthetsedwa kwa mayeso a Fomu 2 kwabweletsa mavuto ambiri pa ana amene asiya kulemba mayeso amenewa. Mavuto awa adza zitadziwika kuti bungwe loyang’anila za mayeso m’dziko muno la MANEB lili ndi ma plan oti tsopano… ...