Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1
Kuthetsedwa kwa mayeso a Fomu 2 kwabweletsa mavuto ambiri pa ana amene asiya kulemba mayeso amenewa.
Mavuto awa adza zitadziwika kuti bungwe loyang’anila za mayeso m’dziko muno la MANEB lili ndi ma plan oti tsopano mayeso a Fomu 4 azikhala ndi mafunso oyambila zimene ana aphunzila Fomu 1.
Malingana ndi chikalata chochoka ku bungwe la MANEB, mayeso a Fomu 4 tsopano azikhala ndi mafunso a zinthu zones zimene ana aphunzila ku Sekondale.
“Paja kale lija timangofunsa za Fomu 3 ndi 4 basi pa mayeso a Fomu 4, koma tsopano zinthu zasintha. Pano tizifunsa zones kuyambila za Fomu 1,” atelo a MANEB mu chikalata chawo.
Zimene a MANEB alengeza zadzetsa tsemwe pakati pa a Malawi amene ali odabwa ndi zilinganizo za MANEB.
Anthu ena amene ayankhula ndi Malawi24 ati zimene akukamba a MANEB ndi zovuta kuti zichitike.
“Koma ngati amavuta mayeso a 4 aja zinthu za Fomu 3 ndi 4 basi, ndiye akanene kuyambila Fomu 1? Apa ayi ndithu apaunikile bwino,” anatelo mkulu wina pothilila ndemanga.
100 thoughts on “Ntchito ilipo pa mayeso a Fomu 4: ati a MANEB azifunsa kuyambila zinthu za Fomu 1”
Comments are closed.

Président wina aliyense abwere busy kuononga maphunziro mmmmm instead of creating jobs aaaaa Malawi at it’s best
Vuto ndi przidnt sakupenya nkuwona kuti kodi school ikupita kuti hahahahah amalawi tonse tagona tulo
Ndimomwe zimakhali sindikudziwa kuti akutathauzanji
Kkkkkk nzeru zatha, instead of making plans to develop the country and create jobs ur busy abolishing Jc hahahahaha, even dogs and cats are laughing at u baba hand over the power if u fail to rule the country and I hope soon u will abolish Msce and next target is University, I never seen a government like this in this planet which kills Education hahahahaha don’t make me laugh.
Kkkkkkk
Why changing things without consulting all people to have a say on the issue. Kupusa pera.
Ohoooo
Survival of the fittest every system has its prons and cons even the present one is not perfect
Ngati mphunzitsi amaphunzitsa subject imodzi basi what about anawa aziwelenga bwanji kuyambira za form one mpaka 4 kkkkk chifukwa zinthu sidzikusitha Ku mw
Koma Kunali bwino akadazisiya kuti mayeso azilembedwa .koma kusitha ndiye kuti mitu yawanafe isithaso aziti oti tizingolowa
Palibe za nzeru apa kufuna kungowalanga ana basi uku mukutolera ndalama…zaziii