Phungu wa MCP wapepesa atanena kuti anthu akumudzi sadandaula za mafuta ophikira
,Phungu wa chipani cha MCP kum’mwera kwa boma la Ntchisi, a Ulemu Chilapondwa, apepesa pa zomwe anayankhula dzulo kuti anthu akumudzi sadandaula za kukwera mtengo kwa mafuta ophikira. A Chilapondwa apepesa lero mu nyumba ya… ...