Abambo atatu apha mzawo ndi zikwanje
Apolisi m'boma la Machinga akwidzinga ndi kutsekera abambo atatu chifukwa chowaganizila kuti adachotsa moyo wa bambo wina wa zaka 60 pomukhapa ndi zikwanje. M'malingana ndi oyankhulira apolisi m'bomali Davie Sulumba, a polisi amangadi John Daudi… ...