Ndondomeko ya mphamvu ku anthu ikuyenda bwino – boma
Boma kudzera mu unduna wa m’maboma ang'ono ndi chitukuko lati ndilokhutira ndim’mene ikuyendera ndondomeko yopeleka mphamvu ku anthu m’dziko muno. Izi ndi malinga ndim’modzi mwa akuluakulu a ku undunawu a Sphiwe Mauwa omwe amayankhula lachinayi… ...