
Apolisi alanda njinga za moto 62 ku Lilongwe
Ngati njira imodzi yofuna kuthana ndi ngozi za pa nsewu, a polisi ku Lilongwe alanda njinga za moto zokwana 62 atapeza kuti eni ake a njingazi amaphwanya malamulo a pa nsewu. Malingana ndi M’neneli wa… ...