Tikakonze malamulo Chakwera apitilize kuposela 2030 – Kathumba
Phungu wa nyumba ya malamulo wa dela la Lilongwe Mapuyu South Esther Cecilia Kathumba ati akapita kunyumba ya malamulo akawupanga mpando wa mtsogoleri wa dziko kuti ukakhale wa muyaya ndipo kuti a Lazarus Chakwera adzapitilize… ...