PAC yapempha a Chakwera kuti achepetse chiwerengero cha nduna komanso alangizi
Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera, apemphedwa ndi Bungwe lotchedwa Public Affairs Committee (PAC) kuti achepetse nduna zake komanso chiwerengero cha azilangi ake ndicholinga chofuna kupulumutsa chuma pamene dziko lino lakutidwa ndi mavuto osiyanasiyana… ...