Kasungu Police

Anjatidwa kamba ka umbava

Abambo awiri omwe ndi akabwerebwere a ku ndende akwidzingidwa ndi apolisi powaganizila kuti amaba katundu osiyanasiyana m’ma nyumba aanthu m’boma la Kasungu. Malingana ndi wachiwiri kwa m‘neneri wa polisi ya Kasungu, Miracle Hauli, abambowa ndi… ...