CAMA yaikira kumbuyo boma pankhani ya mitengo ya yamafuta
Bungwe lomenyera ufulu wa anthu ogula mdziko muno la Consumers Association of Malawi (CAMA) layikira kumbuyo boma pankhani ya mitengo ya mafuta a galimoto. Nkhaniyi ikutsatira zionetsero zomwe zinachitika mkati mwa sabata ino pomwe madalaivala… ...