
A Malawi akusangalala kuno, palibe waombeledwa – yatelo kampani yomwe yalemba a Malawi ntchito ku Israel
Arava Farm yomwe ndi imodzi mwa kampani zomwe zatenga a Malawi kukagwira ntchito mdziko la Israel, yati anthu mdziko muno asadere nkhawa za umoyo wa azibale awowa ponena kuti anthuwa akugwira ntchito mosangala kwambiri, ndipo… ...