Madotolo konzekani: Boma lilemba anthu ogwira ntchito m’zipatala oposera 5, 000
Pamene boma likukonzekera kulemba anthu ogwira ntchito mzipatala zaboma oposera 5,000, mkulu yemwe amayankhulapo pa nkhani za umoyo wayamikira boma la a Lazarus Chakwera kamba kochita chothekera poonetsa kuti anthuwa alembedwe ntchito. Vuto lakuchepa kwa… ...