Odwala ali pa chiophyezo pomwe ogwira ntchito zaumoyo ali mkati mwazionetsero
Anthu ogwira ntchito za umoyo mzipatala zosiyanasiyana mdziko lino ayimitsa ntchito zawo lero ndipo ali mkati mwa zionetsero zofuna kukamiza boma la Malawi kuti liwakwezere malipiro awo. Izi zikudza kutsatira chikalata chomwe wasayinira ndi wapampando… ...