Mabungwe adzudzula amayi oyendayenda omwe amazunza ana awo
Amabungwe omenyera ufulu wa ana ati ndi pofunika kuti malamulo agwirepo ntchito pa amayi oyendayenda omwe amatengera makasitomala awo kuchipinda komwe kuli ana. Bungwe lina lomenyera ufulu wa ana lanena izi poyankhulapo pa zomwe mayi… ...