Ayimba okha apule, a Malawi amenyetsa nkhwangwa pamwala
Anthu ochuluka m'dziko muno akupitilira kukanitsitsa mwantuu wagalu lamulo lomwe walamura posachedwapa mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera kuti nyimbo ya fuko iziyimbidwa ndime zonse zitatu. Lachisanu lapitali a Chakwera analamura kuti nthawi zonse… ...