Malawi24

M’njati wanjatwa!

Apolisi ku Chileka munzinda wa Blantyre, anjata wonyamula mfuti mzawo pomuganizira kuti adachita nsipu wamera mukhola pa mayi wina yemwe adatsekeledwa mchitokosi cha polisi ya Lunzu. Usiku wa Lachiwiri laliwisili, Victor Kachingwe, adachita madyera mphoto… ...