
Boma lati nduna zikhala zikutambasula bwino za zitukuko
Kutsatira mtsutso omwe wabuka pa zitukuko zomwe mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera walengeza posachedwapa kuti boma lake lakwanilitsa, boma lalengeza kuti nduna zikhala zikutambasula bwino za zitukukozi. Malingana ndi kalata yomwe boma latulutsa yosayinidwa… ...