A Malawi akunyinyilika Wode Maya atatchula mbewa kuti soseji
Inde mlendo Wode Maya wadza nkalumo kakuthwa, komatu wadzetsa kung'ung'udza m’masamba anchezo pa mpanje pano kaamba koti waliuza dziko la pansi kuti ku Malawi kuno mbewa zija ndi makoswe komanso akuti ‘makoswewo' timawatchula kuti soseji… ...