
Zayang’ana kungolo, Calista agwa kuzisankho zachipulura
Yemwe anali mkazi wa mtsogoleri wa kale wa dziko lino malemu Bingu Wa Mutharika, Calista Chapola, akudziguguda pachifuwa pomwe wagwa chadodolido pa zisankho zachipulura m’chipani cha Malawi Congress. Chapola adasamuka mchipani cha Democratic Progressive (DPP)… ...