Ulendo wa ku CAF watalika kwa nyerere: ayamba kupemphetsa
Onse okonda nyerere ndi akufuna kwabwino, sonkhani limodzi limodzi kuti ulendo wa akatswiri a ligi opita ku CAF asauyende wapansi. Wa ana a Israeli mu chipululu. Ngakhale anakwela pachulu, kuziguguda pa chifuwa kuti iwo zivute… ...