A Mutharika akana kufunsidwa mafunso ndi ACB
Mtsogoleri wakale wadziko lino a Peter Mutharika akana kufunsidwa mafuso ndi bungwe lotsogolera ntchito yothana ndi katangale la Anti-Corruption Bureau (ACB) pankhani yakugwiritsidwa ntchito kwa nambala yawo ya TPIN pakugulidwa kwa simenti. A Mutharika amayenera… ...