A Nankhumwa ati boma lichotse misonkho pa mafuta a galimoto
Mtsogoleri wotsutsa boma a Kondwani Nankhumwa alangiza boma kuti lichotse ina mwa misonkho yomwe inayikidwa pa mafuta a galimoto ponena kuti ndiyomwe ikupangitsa kuti mafutawa akhale okwera mtengo kwambiri. A Nankhumwa amayankhula izi atayendera ina… ...