MCP ithibula DPP mu zisankho zapadera
Chipani chotsutsa cha Kongeresi chaonetsa mbonaona chipani cholamula cha Democratic Progressive mu zisankho za padera zimene zinachitika mu madera asanu a dziko lino. Chimake cha zisankhozi chinali ku Mchinji kumene amasankha phundu wa nyumba ya… ...