‘Koma ali ndi umunthu abusawa?’ – a Malawi adabwa ndi ulendo wina wa a Chakwera
Pamene anthu akugona pa malo omwetsera mafuta ndipo dongosolo la fotereza silikulongosoka kamba ka kusowa kwa ndalama za kunja, a Chakwera akuotcha mtambo mawa lomweli. Khalidwe limene ladabwitsa a Malawi ochuluka. Atangotha masiku kubwera kuchokera… ...