Aphunzitsi awopseza kuti ayambilaso sitalaka
Aphunzitsi m'dziko muno awopseza kuti ayambilaso kunyanyala ntchito ngati kwa masiku asanu ndi awiri (7) akubwerawa boma silipanga zomwe anagwirizana kumayambiliro kwa mwezi uno. Pa 8 March chaka chino boma kudzera ku unduna wazamaphunziro linagwirizana… ...