A Mutharika sanayenera kujomba ku msonkhano wa AU
M’modzi mwa akatswiri pankhani za ndale m’dziko muno a Wonderful Mkhutche ati mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika mwanjira ina iliyonse anayenera kupezeka kumsonkhano wa atsogoleri maiko a mu Africa. A Mutharika sanakhale nawo… ...