‘It was the fault of the Police’ – says Stadium stampede survivor


Stampede

One of the children who survived the Bingu National Stadium stampede has faulted the police for failing to control the situation professionally.

The boy who did not want to be named said police officers fuelled the commotion at the stadium when they began beating people as a way of stopping them from entering the stadium after the gates were opened.

“Police officers were fighting people because of the overcrowding at the gate. As a result of this some people especially children fell down that forced others to step over them,” the young man told Malawi24.

Stampede
Police blamed for the stampede.

“Police officers are to blame because they used violent measures of cooling down the situation. Had it been police officers used proper measures, the incident would have been avoided.”

He then thanked God for saving him saying he was smelling death.

Eight people died in the stampede of which six are boys while the other two are a girl and a man.

On Thursday afternoon, President Peter Mutharika visited people who got injured due to the stampede and spoke on the need for authorities to make sure that such a tragedy should not happen again.

“Authorities should make sure that this does not happen again,” said Mutharika. “These are modern facilities with the ability to accommodate a number of people.”

156 thoughts on “‘It was the fault of the Police’ – says Stadium stampede survivor

 1. Kalekale 6july kamuzu stadium imasegulidwa 5pm pa 5july. Imakhala yosekula mpaka 10am pa 6july. Iyi mukusekula masana,zaulerezo? Ose anali my organising committee aimbidwe mlandu. Kupanda teargas pakadafa anthu 89+

 2. Parents at one point lets try to protect our children, in such occasion we can’t lets under 12 children to attend that ceremony, where ever there is free of charge occasion people especially young one get mad, we as parents we must be carefully of what we are doing to our children

 3. Mudzaziona apa mukulankhula zofoira chifukwa zachitikira anzanu. Simukudziwa mmene situation inalili and u don’t know how that teargas saved others. It’s your right u can talk to the maximum.

 4. Kod patsikuli chimachitika ndi chani?…If you say don’t blame the police, what were the duty of police on that day to let the people being killed by each other neither to control crowd

 5. A Malawi taganiza m’mene able and alongo athu a mwalllira in the months of June and July pangozi zosiyanasiyana.mwina mwaketu wina akupereka nsembe.Ai ine ndazizwa nalo dzikoli.

 6. Blame the DPP gvt becoz even if u change the gvt nw it wil b the same police. Munthawi ya MCP magate amkatsegulidwa one week before 6 july vuto lomwe limkakhalako anthu amkasokera munthu waku nsanje amkapezeka wakwera bus yaku mzuzu

 7. Kodi a police akanachita control yanji polesa anthuwo kuti asakwele mpanda ,munangakhala kuti ndinu modzi wa a police mukanagwilitsa njila yanji tiudzeni timve nzeru yanu chifukwa musamango zuzula musana peleke nzeru yomwe munangagwilitsa ntchito munangakhala kuti ndinu wapolice?

 8. The big stadium with only 1gate that people can use why?ukeep 7gate to use vip other poor people use one gate ujust show ur stuppid government.those people by two much she/he must get there compasation money for fatal death

 9. What other method police would use apart from firing teargas? Blame them if at all are responsible for gate controlling coz the gate was opened very late.

 10. I give my blame to Stadium authorities had it been kuti anatsegula mwachangu ma gate ngati mmene akhala amapangira kumboyo pa Kamuzu Stadium sizikanachitika zonsezi

 11. It was management error, not police. The gates should have opened much earlier on. In developed countries management would have resigned or face the chop……… ..and face MANSLAUGHTER charges.

 12. You will see the will get away with it without any action taken on them! most of the people that we have experienced this before we know its true! I mean Malawian police beating people using the power of being policemen will agree with me! No wonder at 53years of independence there is nothing to show!

 13. The prblm with our plc z they think every prblm can be solved using teargas,if they don’t adapt new ways of crowd control this will be our daily results.

 14. My question is. Why did they had to wait to open the gates at around 11 when the cloud was there from around 8. If they gates were open early enough, maybe at 7 all this wouldn’t have happened. But the police guarded the gates till the cloud was too much and it went out of control. Next time when such events are happening do not close the gates cause it’s a free event. Everyone wanted to be early to get a good spot in the stadium. Police and the organizers failed to see that through when the place started to cloud with people. Especially kids!

 15. Ths is case for gate man why thy didn’t open very early kuti anthu the moment afika azilowa kopanda vuto .to my self I blame the people thy control gates .why thy don’t open early

  1. Ndiponso zosenzi zachitika kopanda dongosolo abale zoona akuwona kuti pali ana bwanji akanapanga mwaulemu, ifenso tilikuno kunja sikwathu koma amalemekeza ana tikapita kuhome affairs

  2. We can blame the police officers but let us blame ourselves, AmaLawi tisayembekezere chikhalidwe kuti apolice azitiphunzisa always, e.g pokwera taxi or bus kumene, zimakhala zopanda dongosolo, kulandira kumene zinthu za ulere palibe zadongosolo, ena mpaka amayesesa even kulandira 2 to 3 times, bwanji wosapanga line?or pokwera ma taxi tizifikila pa line we can’t wait for gvt to tell us what to do

 16. Apolice sitiwaopa!!! Next tym! Kuzakhale asilikali!!!!! Nde mumaziwanso maguyz amene aja2!!!!! Nkhaza nde amalawi timafuna!!! Kudekha mkumvesesana ai sititha!!!! Kunakakhala kt kb sina2mize anthu ake eish!!!!!!!! Kunakakhala zachison heavy!!!!!!kuposa zaonekazi

 17. Human beings are often good at blame-shifting. They don’t want to recognise their contribution whenever something wrong/bad happens.

 18. Our Stupid Police must b taught how or when to use Tear Gas. They new very
  well that children were also in the stadium. But they fired tear Gas.

 19. Chinapangitsa zonsezi ndi mphavu ya satana inazera mwa a police ndi oyang’anira stadium blame that satan we should pray to the lord almighty

 20. Kodi anthu amene mukunyoza apolisi muli ndi ukadaulo wanji wokhazikitsa bata gulu la anthu loti likuchita chisokonezo. Don’t just say eee apolisi akumalawi sadziwa ntchito yawo as if you better to control the crowd. Firing of tear gas was the most effective and efficient way of avoiding more deaths. If you think that wasn’t the best technique of controlling people who were scrambling and panicking to gain entry what other methodology would have been used to control them?

  1. @Rafick Aca Black China what u r saying is not applicable. U r talking of mic phone that would have taken long for people to respond hence more deaths. Tear gas was the only viable means of stopping the stamping of people who had fallen down.

 21. Yes polices fault umbuli kwambiri kumalawi wakagwilitsidwe ka tear gas ⛽️ kaya amaona like zosangalatsa kumangoponya gas ⛽️ paliponse umbuli ndi Ana omwe.

 22. A police Aku Malawi Ndixitsilu Za Anthu Kwambir M’malo Mogwila Ntcito Yawo Mwamtendele Amalimbana Ndkupanga Zopusa Zaozo…………Nkhan Yosaenela Kuponya Utsu Okhetsa Nsoz Iwo Ndpomwe Amaponya Kaa Amasowa Zoseweletsa…………….Taonan Mwaphetsa Ana Ang’ono Ang’ono Osalakwa………..Ucitsilu Mudzasia Liti Kod Anyapapi Inu??

  1. Mukanakhala kuti munali ku BNS mwina mukadayamikako kuti teargas mukumudalo saved many more pple from death. Teargas anathandiza kupanga disperse anthu omwe amangopondana so that the police shud help those amene anavulala….., koma poti a police timadana nawo ndikale, we end up making comments like these. Why not blame the stadium authorities for opening the gates late? Kapena a police ndi amene amayeneranso kutsegula ma gatewo?

  2. Anthu anayenela kukhala panzele mwadongosolo zimenezo akanachita m’mamawa womwe uku chitetezo chili chokwima koma anthu anangowasiya ngati mbuzi akanatani kupondana basi

  3. Naweso uziyankhula za fundo ngat Bambo a police zisiru olo stadium ukuyiziwa iweo za ziii ufuna kupeza potchukira ndifundo yama tewe yi

 23. Thise police,the Are not professional sadziwa kupanga handle anthu opanga chisokonezo kapena malo mwa anthu ochuluka.ubuli wawoo ndiumene waphetsa anthu,fools

  1. Thats not true my friend
   Upite dziko lilose aise pomwe anthu ochuluka asokhana wa police ntchito yake imakhala yowawa kwambiri komaso ngati akupanikizana mpovuta kupanga control zinthu zotsatila zake ndi zomwe za chitikazi so if u want to put blame on cops I think upiteso ku xul
   And by the way I think training yao akuyenera kupha kuti ateteze

  2. MAYI INU NDE MUMATHA? Amalawi ena alind usavage thoooo! Ngat mupitirixE kupañga blame a police mutafe ndinu iwo aligwa

 24. i dis agree,because iwent there too the police fired teargas when the stamped has arleady hapened if teargas was not fired at that paticular tyme many people could hav died,when teargas was fired people withdrew from pushing each other giving chance to those who were down wounded,some tymes dont just blame the police for the sake of blaming.i too blame the police when they did wrong but on this ngoooo!.idont think the police wronged.i was there myself.

  1. Mumango kuthilila ndemanga pakuti afawo p palibe wakubanja kwanu muziganiza bwino mutakhala kuti abale anu ali khulu la anthu afuwawo.Amalawi bwanji kupanda chifundo

  2. phunzilani kunena zowona,osamangowonjezela nkhani kuti mutchuke,mmodzi mwa anthu ovulala ndine,iwas at central hospital yesterday ndipo pano ndikupezako bwino kupanda apolice kuthila teargas ifenso tikanafa chifukwa chigulu chonse chikanatiponda,ndingoti zikomo ambuye.

  3. Kuno ku Malawi mpovuta kuti anthu ayamikire ntchito za apolisi. Very rear. I don’t know why there is this much hate against the police by the public. Ngakhale olemba nkhani amapotoza dala nkhani kuti apolisi aoneke olephera nthawi zonse.

  4. Man bwanji mukubakira zinthu zapunsa gati yinzi kapena pa gulu la police wo pali m’bale wanu? apa ndizowonekelatu kuti apolice adakanika kungwira ntchito yawobwino

  5. Komadi munthuyu mumvetsetse.Inenso ndinali mkatikati mwa chipiringucho kungoti mwayi wake sindinage pansi koma kunena chilungamo,akanapanda kuchotsa anthu mwachangu tikadafapo ambiri n za tear gas zo ine sindinazione coz pamene timalowa panalibe kuthira tear gas kwina kulikonse mpaka pamene anthu anayamba kumagwetsana,kusonyeza kuti tear gas wathiridwa pambuyo.

  6. I was in Durban yesterday. Just arrived home this morning. Am sorry for the loss of more than 8 children. Those in hospital, am wishing them a quick recovery….. Let us stop BLAME GAME!!!!

  7. Is true to blame the police bcoz they failed to calm situation at first then spread teargas when things already worse,teargas add up fuel as ppe we’re trying to run from it

  8. I blame the police too why did they fail to control the situation??? And throwing teargas is prohibited and throwing teargas at kids that’s worst thing to happen cz they inhale them and its disastrous

  9. who told you that teargas is prohibited . Martha zimenezi ndiye zida zogwiritsidwa ntchito ndapolisi komaso muveseseni akhristu momwe wakambira, wanena kuti popanda kuponya teargas anthu akadafa ochuluka . Police ndi ntchito amachita kufusira ndiye kaya enanu anakusiyani sanakutengeni mtima mmalo Mulungu wakukozerani mbali ina koma ichi chisakhale chifukwa chosambwadzira apolisi.

  10. Let’s not point fingers, AmaLawi tili ndi vuto lalikulu, sometimes tingaziteteze tokha without a police, e.g pokwera taxi, zopanda dongosolo even polandila zinthu za ulere sipamakhala za ulemu, ena akalandila even 3 times, akuti kuchenjera which is not good, we can avoid these problems ourselves not police, pokwera taxi tizifikila pa line, polandila za ulere let’s make a line so that we can avoid this problem.

  11. firering teeagas is that protection???!kapena you are one of the salvage police?who were thea?you dont na how life cost my dear,just keep quite

  12. firering teargas is the only gud solution at the moment rather than live ammunitions,the stadium director openly said on zodiak that the blame shud go to him and oganisers for not opening gates in time,he said police are not to blame.may be u dont understand teargas was fired after the stamped to avoid people steping on the wounded who were arleady down.what about people who steped on other pipo did they do the wright thing,everybody cares about lyf,if u care much why dont u go to the hospital to sheer them.world wide police is not loved more especially evil doers.

  13. In short anthu inuso munali pachigulu nanu munaganiza bwanji. Why couldn’t you wait in a proper order to get in. But still we blame police cause they failed to maintain order in the first place before zonsezi. Teargas makes people weak!

  14. Iwe wezzie kunzimva ku phunzila kwa mbiri iweyo?? Uganize nambala ya anthu omwe anali kumene kujako,, ndi nambala ya apolice omwe analikowo zimagwilizana?? Anthu tilipo ambili apolice ndi ochepa.. Kumayamba mwaganiza kaye musanalankhule ndikuphunzila kwanuko..!!!!

  15. Akutelo kunziva kuzindikila heavy kkkkkk!!!!!koma choti adziwe ndichakuti anakapanda kuponya teargas,anthu akanafa ochuluka kwambili ndimmene zinalili.a police anali ochepa ndimmene anthu analili komabe anayesetsa don’t blame the police pliz!!!!

 25. Kodi Mulibe Nkhan Zina Zoti Mupangat Post? Nkhaniyi Yatikwana! Vuto Ndi Anyawu, Eti Mmene Yakulira Stadium Muja Mpaka NKumalimbirana Kulowa! Zawo Izo

  1. Khala ndi umunthu man, moyo wako siwamuyaya and you don’t know how you will die. Imfa yako ikhoza kudzakhala yowawa kwambiri. Za maliro osamazitengera zibwana. Ife tikulira abale athu and you are posting shit here, why can’t you just keep quite.

 26. Apolice aku malawi ali ndivuto kwambir kaya ndi aja othawira pa window ku xul ma why are u felling to control such kind of situations but u know that end result z accidents pliz muziyesesa koma

  1. So with this English u have the guts to mock police that they are school dropouts? Anyway may the souls of the departed rest in peace.

  2. Enanu mukukamba ngati kuti inuyo mukanakwanitsa kuongolera chikhamu cha anthu mwa myaaa !
   Tithandizane kupereka mfundo zothandiza kuti zoopsa zoterezi zisamachite. Osati kunyozana, kulalatirana kapena kutukwana.

  3. Taonga myankhata…who will need the Police?? a police ake aku malawi a mbwii wa?nkhani corruption,chitetezo gooo,cant you feel sorry,va police vili pompo anthu kumafa whats that?chitetezo chao chili pati??? amakataniko?ndiye?koma inu zimavetsa chisoni that wa police yo naye ali gulu lolowa moteremo,thats y,people calls them salvages

  4. Wezzie chepesa kulankhula chipongwe… Ndipo ngati ndiwe ophunziladi kwambiri koma apapa pali cha nzeru chomwe ukukamba chifukwa zikuoneka kuti ukungolankhula usanaganize…. Ndipo dziwa kuti ukakwera mumtengo usanyoze wa pansi…. (educated savage)

  5. wezzie its God who protect everyone olo iwenso amakuteteza ndi mulungu apolice amangothandizila nawo ndi anthu ngat iweyo. samalani pakamwa panu mayi , ngati muli ophunzira muli pa ntchito yabwino yamikani mulungu, if you read the Bible it says there is time to born and time to die amenewo nthawi yawo inakwana

  6. Komano ndazitolera vuto si apolice ndi koma amene amayang’anira bwaloli ndamene anapanga zofoirazi vuto ndichani kaya

  7. Tawonga and your frens simungandiopseze,mbuzi za anthu,kodi wa police akati wa police ntchito yake ndi chani? mukunya mwano poti si abare anu,that is y mukunya mwano, abare awo awanthuwa akumva ululu,YES IKNOW AMATETEZA NDI MULUNGU,KOMANO THE SAME GOD ADATIPATSA BRAIN,THAT WE SHOULD USE IT FOR PURPORSES,THAT IS Y,ENANU KULI A POLICE OSATHANDIZA Zakuwawani.poti ndinu savages

 27. Ana amataniko kuzinthu ngati izi kopanda owasogolera bwino kumapezeka kuti mwina ndi aja ana amapemphesa muma robot chifukwa m’mene anawo akuonekera zikuonesa kuti owasogolera panalibe monga ngati makolo kapena azibale awo ena

 28. I can agree that a police akuno satha kupanga handle zinthu, amaponya teargas pa zinthu zosayenela kuponya or palibe chisokonedzo,

  Komaso zinthu zaulele ndi chifukwa chani chosekula ma gate mochedwa chikhalileni ndi independence

  1. Anthu akulowa palibe zipolowe akuthamangila mmipando apeze pokha choponyera teargas mchani ndiwe mbuzi aPolice ambili saidziwa ntchito yao

  2. I agree with you Moses Kambwiri. Ena akanyoza, akatukwana, akalalata, zawo zimakhala bwino, mmalo mopereka mfundo zothandiza.

Comments are closed.