Gulu lakale la Payoniya liopseza kuchita m’bindikiro mwezi uno
Anthu omwe anali a Payoniya mu ulamuliro wa chipani chimodzi cha Malawi Congress omwe mtsogoleri wake anali malemu Hastings Kamuzu Banda awopseza kuti achita m'bindikiro ku ma ofesi a boma Capital Hill ngati boma siliwalipira… ...