Ya ma 1 pin a ku chipatala yavuta
Ena akuti ikumveka ngati ya ma kadi ija a Malawi anaikana pa dzana mu ulamulilo wa Kongeresi. Ena akuti tisakambilane iyiyi pamene tikukanika kulimbana ndi katangale. Otakasika ena akutsindikanso kuti imeneyi ibwele ndithu, pasakhale munthu… ...