Nkhani ya ma kondomu achikazi ivuta: amayi akuwakana ati amaononga chisangalalo
Akatswiri pa nkhani ya uchembele wabwino adandaula kuti ma kondomu achikazi sakugwilitsidwa ntchito pamene zikuoneka kuti anthu achizimayi akuchita chowazemba. Izi zaululika pa msonkhano wina omwe unachitika mu boma la Mzimba. Poyankhula pa msonkhano umenewu,… ...