Mvula iyamba lachisanu, atero a zanyengo
Nthambi yowona zanyengo ndi kusintha kwa chilengwedwe yati mvula iyamba kugwa mdziko muno lachisanu sabata lino. A Jolam Nkhokwe omwe ndi mkulu wa nthambiyi ndi omwe anena izi polankhula ndi wailesi ina mdziko muno. Malingana… ...