Anthu a ku Chingale achita m’bindikiro ku ofesi ya Zomba Escom
Anthu ochita malonda ochokera kwa Chinseu m'dera la Zomba Lisanjala anachita m'bindikiro ku office ya Escom mu mzinda wa Zomba powonetsa mkwiyo wao kuti akhala miyezi isanu opanda magetsi potsatira kupsa kwa transformer mdelaro. Poyankhula… ...