Depoti ya Balaka yayambiranso kugwira ntchito yake
Patapita zaka pafupifupi zisanu malo okwelera galimoto pa tawuni ya Balaka asakugwira ntchito, adindo m'bomali tsopano alengeza za kuyambiranso kugwira ntchito kwa malowa. Bwanamkubwa wa boma la Balaka, Tamanya Harawa watsimikiza kudzera mu chikalata kuti… ...