Hellen Singh
Mmodzi mwa yemwe adapikisana nawo pa mpando wa utsogoleri m'dziko la Malawi pa zisankho za m'chaka cha 2014 mayi busa Hellen Singh amwalira usiku wa loweluka. Mayi Singh omwe anali mtsogoleri wa chipani cha United… ...
Midori
Ngakhale bungwe loyeza zakudya m'dziko muno la Malawi Bureau of Standards (MBS) lidaletsa mowa wa mmabotolo a plastic, mowawu ukupezekabe pa msika mma boma ambiri mdziko muno. Diso lakuthwa la Malawi24 lapeza kuti mowawu omwe… ...
Bambo wina m'boma la Machinga wamwalira atavulazidwa mochititsa mantha ndi Njati yomwe inathawa ku malo osungira nyama za mtchire a Liwonde m'bomalo. Malingana ndi oyankhulira apolisi ku Machinga Davie Sulumba, mkulu waphedwayu ndi a Steward… ...