Manyi ali khathikhathi m’madzi akumwa ku Lilongwe

Bungwe la madzi la Lilongwe Water Board (LWB) laulula kuti madzi omwe anthu akuyenera kumwa mu mzinda wa Lilongwe mukupezeka manyi ochuluka ngati a mu suweji.

Mkuluyu wa bungweli, Alfonso Chikuni, ananena izi pomwe anakumana ndi ma membala a ndondomeko yowona za chuma ku Nyumba ya Malamulo.

“Muli manyi akhatikhati mu madziwa mwakuti palibe kusiyana kwenikweni ndi ku suweji,” anafotokoza motero a Chikuni.

Bambo Chikuni anati bungweli likuononga ndalama zankhaninkhani kuyenga madziwa kuti afike pa mulingo oti anthu nkumwa popanda chiopsezo pamoyo wawo.

Advertisement

903 Comments

 1. Nde wina aziti atonga amanyera mmadzi, apa nde zachita kuonekeratu a………naoso amanyera mmadzi.ndimadabwaka kuti madzi ochokera pampopi amaveka zinazake mmmmmh.

 2. Nde wina aziti atonga amanyera mmadzi, apa nde zachita kuonekeratu a………naoso amanyera mmadzi.ndimadabwaka kuti madzi ochokera pampopi amaveka zinazake mmmmmh.

 3. I thank we hav to undertand dat these r very old pipes. Thats y government whats to pump water 4m lake MW. Find some people they r puting obstacles to dely this as if its only government which will benefit. What z politics z this???? Many politicians n mw thinks dat the word ‘NDALE’ z to make someone fall down,thats why they opposing things that will help their health.

 4. I thank we hav to undertand dat these r very old pipes. Thats y government whats to pump water 4m lake MW. Find some people they r puting obstacles to dely this as if its only government which will benefit. What z politics z this???? Many politicians n mw thinks dat the word ‘NDALE’ z to make someone fall down,thats why they opposing things that will help their health.

 5. Eeeh ife timadabwatu anzathunu matupi kusalala ku town, ife nkumangotinamiza kuno kumudzi ati mudzidya zamasamba ndi zipatsa, ife kumafa nawo nkhwani wa dayile ft matowo ndi nthudza ngati zipatso konsekotu kufuna kusalara ngat akutawoni kani ndie nkhani yake ati. Mmatibisilatu chinsisi eti, Ife ndi mchimidzimidzi busy ndi madzi apachitsime a chule akujowa mbalimu apo kasi niyamene..ayi mwatiwuzako timasowekera uthenga wabwino ngati umenewu ifeso tiwona mmene tichitire kuno mzitsimezi. Mwina tingayambepo kufanana apa..alaaaaah shupiti

 6. Eeeh ife timadabwatu anzathunu matupi kusalala ku town, ife nkumangotinamiza kuno kumudzi ati mudzidya zamasamba ndi zipatsa, ife kumafa nawo nkhwani wa dayile ft matowo ndi nthudza ngati zipatso konsekotu kufuna kusalara ngat akutawoni kani ndie nkhani yake ati. Mmatibisilatu chinsisi eti, Ife ndi mchimidzimidzi busy ndi madzi apachitsime a chule akujowa mbalimu apo kasi niyamene..ayi mwatiwuzako timasowekera uthenga wabwino ngati umenewu ifeso tiwona mmene tichitire kuno mzitsimezi. Mwina tingayambepo kufanana apa..alaaaaah shupiti

 7. Lake Malawi Madzi Ambili ..koma Dyera Lachuluka kwambir Ku Pa Top official… .Ma yield A Dyera AmeneWo…Tiyeni naxo & I wish that pipe inali yopita Ku state House

 8. Lake Malawi Madzi Ambili ..koma Dyera Lachuluka kwambir Ku Pa Top official… .Ma yield A Dyera AmeneWo…Tiyeni naxo & I wish that pipe inali yopita Ku state House

 9. Aaaa ine I don’t see any problem with that, more over we malawians we don’t even know that those manyi thngs r very much important in our bodies

 10. Aaaa ine I don’t see any problem with that, more over we malawians we don’t even know that those manyi thngs r very much important in our bodies

 11. This post is Slanderous and a disgrace to the entire Journalism Industry. I don’t think it passed through the Editor. Parrots!!!!!!

 12. This post is Slanderous and a disgrace to the entire Journalism Industry. I don’t think it passed through the Editor. Parrots!!!!!!

 13. Ha ha ha ha!!!! anthuakulilongwe kunyadakosekunja zoon mot mumadyamanyi ??? zomvetsachisonikwambili mpakana akhathikhathi ngat phala ? mwinand break fast yanu yamamawa uliose.

 14. A LL Water Board alakwitsa kuulula nkhani imeneyi akhumudwitsa anthu, bola kumamwa usakudziwa iwo nkumangolimbikira kuwachita treat madziwo basi. Moti nawonso akumwa nawo omwewo?

 15. A LL Water Board alakwitsa kuulula nkhani imeneyi akhumudwitsa anthu, bola kumamwa usakudziwa iwo nkumangolimbikira kuwachita treat madziwo basi. Moti nawonso akumwa nawo omwewo?

 16. Kkkkkkkk.names changes , water board to manyi board & water bills to manyi bills Kkkk madzi house to manyi house. Moti dollar ndimavutikila kuzipezamu ndimalipila manyi?

 17. Kkkkkkkk.names changes , water board to manyi board & water bills to manyi bills Kkkk madzi house to manyi house. Moti dollar ndimavutikila kuzipezamu ndimalipila manyi?

 18. Ndie mwati zaka zonsezi takhala tikumwa zimadzi za manyi akhathikhathi!! Zachamba sindibwereranso nsanga ku lcity am safe here ndidikire kae a lake malawi.

 19. Ndie mwati zaka zonsezi takhala tikumwa zimadzi za manyi akhathikhathi!! Zachamba sindibwereranso nsanga ku lcity am safe here ndidikire kae a lake malawi.

 20. and am sure its not only Lilongwe nooo ndidapitako ku Liwonde water treatment plant up to this day sindidamwenso madzi aku Liwonde ishiiii bibi yokhayo nde amacita kunena kuti mmm we will purify osadandaula ishiiiii nde was thinking nanga BT,LL with mitsinje yonyasa ija mmmmm

 21. and am sure its not only Lilongwe nooo ndidapitako ku Liwonde water treatment plant up to this day sindidamwenso madzi aku Liwonde ishiiii bibi yokhayo nde amacita kunena kuti mmm we will purify osadandaula ishiiiii nde was thinking nanga BT,LL with mitsinje yonyasa ija mmmmm

 22. Mmmm interesting nd I’m so in love with the language wish I can hear u guy’s.Im jst smiling to all yr comment even though i im nit hearing what u say,Any volunteer to teach plzzz

 23. Mmmm interesting nd I’m so in love with the language wish I can hear u guy’s.Im jst smiling to all yr comment even though i im nit hearing what u say,Any volunteer to teach plzzz

 24. Bola mukana lemba muchilomwe zikanapepukako koma izi zakhumudwisa anthu ambili ngakhale anthu ogulisa mazi mumisewu azi wonangati akugulisa mazi amanyii

 25. Bola mukana lemba muchilomwe zikanapepukako koma izi zakhumudwisa anthu ambili ngakhale anthu ogulisa mazi mumisewu azi wonangati akugulisa mazi amanyii

 26. Kuzolowela kuwayetsa anthu umve basi, Mpakana manyiiiiii khathikhathi man M mmm ayi zawonjeza ku Malawi, Mpakana manyi ndithu??? Sheeeeeeeeeh vutono ndi kukhala chani kwenikweni? ?? Madzi atha kapena??? Ndeno mwati bolaniko anthuwa adyeko manyiiiiiii M mmm umve basi.

 27. Kuzolowela kuwayetsa anthu umve basi, Mpakana manyiiiiii khathikhathi man M mmm ayi zawonjeza ku Malawi, Mpakana manyi ndithu??? Sheeeeeeeeeh vutono ndi kukhala chani kwenikweni? ?? Madzi atha kapena??? Ndeno mwati bolaniko anthuwa adyeko manyiiiiiii M mmm umve basi.

 28. Where is the government if this is really true deal with the water board why laughing comment Magayi be serious I can assume there is no security at waterboard

 29. Where is the government if this is really true deal with the water board why laughing comment Magayi be serious I can assume there is no security at waterboard

 30. kkkkkk Ine kudabwa tikayendela achibale ku LL madzi ake amaveka zinazina,Kani zinali zimenezo,mmmm ai tikamapita kumeneko tiziyenda ndichigubu chamadzi.

 31. kkkkkk Ine kudabwa tikayendela achibale ku LL madzi ake amaveka zinazina,Kani zinali zimenezo,mmmm ai tikamapita kumeneko tiziyenda ndichigubu chamadzi.

 32. Aaaaaaaaaaa!!! Anthu kunyela mipwelele zaka zonsezi, ife kumati ndi Edzi koma mukuwapweteka ndinu a Boma, water board ikufinika kugamulidwa mlandu..

 33. Aaaaaaaaaaa!!! Anthu kunyela mipwelele zaka zonsezi, ife kumati ndi Edzi koma mukuwapweteka ndinu a Boma, water board ikufinika kugamulidwa mlandu..

 34. kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk baaaaaaaaaaaaaad this is very baaaaaaaaaaaaad indeed baaaaaaaaaaaaad kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

 35. kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk baaaaaaaaaaaaaad this is very baaaaaaaaaaaaad indeed baaaaaaaaaaaaad kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk

 36. Ku State House,ku Parliament, Area 43, Ku Mchesi Tonse Tikumwa Manyi Okhaokha 4 Now 5o Years Tikudzilamulira Koma Manyi Basi.Water Boad Osamangothamangira Kudula Madzi Amanyiwa Ayi Tidzakugendani Tatopa Ife Mumve.

 37. Ku State House,ku Parliament, Area 43, Ku Mchesi Tonse Tikumwa Manyi Okhaokha 4 Now 5o Years Tikudzilamulira Koma Manyi Basi.Water Boad Osamangothamangira Kudula Madzi Amanyiwa Ayi Tidzakugendani Tatopa Ife Mumve.

 38. EIA iz just useless to on pumping water from the lake , water is life you don’t compromise with water, why delay ? If it was uranium mining I would say yes but water and pipes from the lake what effect would it have on environment ? Leave this brain child to the one who has pioneered it , it will go in history for the first time in Malawi pumping water from lake Malawi to upland like Lilongwe let’s support it. Kamuzu dam 1and 2 are drying up plus siltation it needs dredging which is not an easy job. You can’t see this , one day you will wake and see Lilongwe has completely no water , we to focus and have vision we can’t wait for donnorz to do this for us any more iyaah!

 39. EIA iz just useless to on pumping water from the lake , water is life you don’t compromise with water, why delay ? If it was uranium mining I would say yes but water and pipes from the lake what effect would it have on environment ? Leave this brain child to the one who has pioneered it , it will go in history for the first time in Malawi pumping water from lake Malawi to upland like Lilongwe let’s support it. Kamuzu dam 1and 2 are drying up plus siltation it needs dredging which is not an easy job. You can’t see this , one day you will wake and see Lilongwe has completely no water , we to focus and have vision we can’t wait for donnorz to do this for us any more iyaah!

 40. Difficult time, I wish people should be happy as long as they are healthy and strong, you will never vomit things you swallowed already be safe and trust yourself by boiling the water, can eliminate germs that might cause deadly deases.

 41. Difficult time, I wish people should be happy as long as they are healthy and strong, you will never vomit things you swallowed already be safe and trust yourself by boiling the water, can eliminate germs that might cause deadly deases.

 42. Koma chichewacho mwawonjedza bolanso mukanalemba kuti matuvi. Ku state house komanso ku Parliament tonse tikumwa madzi ake omwewa

 43. Koma chichewacho mwawonjedza bolanso mukanalemba kuti matuvi. Ku state house komanso ku Parliament tonse tikumwa madzi ake omwewa

 44. Nkhawa njee…!TIMWE BAS, CHINANENEPESA NKHUMBA SICHIDZIWIKA.. Chris Taddy Nazombe Wixy Chicox Wadi Chisoni Kapalamula Hezrhone Mbizi Pauline Kachambo Khudze Gift Prisca Jim

 45. The people who are working at Water Board full time, what are they paid for? Are they ghost workers? Otherwise they must be expelled and hire dedicated qualified workers to do the job. The people have the right to sue the Water Board for compensation of money spent for medicine and doctors for sickness caused by affected water.

 46. The people who are working at Water Board full time, what are they paid for? Are they ghost workers? Otherwise they must be expelled and hire dedicated qualified workers to do the job. The people have the right to sue the Water Board for compensation of money spent for medicine and doctors for sickness caused by affected water.

 47. anthu tonse amene timadya somba michimba ya anthu komaso timinofu ta anthu ofera mmadzi timazidyera limodzi,cholowa sichiipitsa munthu koma choturuka bora moyo.

 48. anthu tonse amene timadya somba michimba ya anthu komaso timinofu ta anthu ofera mmadzi timazidyera limodzi,cholowa sichiipitsa munthu koma choturuka bora moyo.

  1. Mumanyela mmazimo ndiinu nomwe nde simungadwale. Koma mmene mwaziwapa akupwetekani mazi [email protected] ndi a pitala omwe amamwa nawo @@ndimadabwa kukamba wamba nthawi zambili MABI amakhala akulowelela mpaka muubongo.

  1. Mumanyela mmazimo ndiinu nomwe nde simungadwale. Koma mmene mwaziwapa akupwetekani mazi [email protected] ndi a pitala omwe amamwa nawo @@ndimadabwa kukamba wamba nthawi zambili MABI amakhala akulowelela mpaka muubongo.

 49. Thus ur work bwana Chikuni to remove those n xul yanu ija ndi anyamata anuwo mumapitira zimenezo. A Simbi can’t proceed if simuyankhulako coZ u have da key as katswiri wa ncthitoyo

 50. Thus ur work bwana Chikuni to remove those n xul yanu ija ndi anyamata anuwo mumapitira zimenezo. A Simbi can’t proceed if simuyankhulako coZ u have da key as katswiri wa ncthitoyo

 51. Boma likufuna kukukokerani madzi from lake malawi kuti mumweko fresh water osati zigayigayi mukumwazi zakumalingunde zomwe amakala abibira, koma inu ati kudziwa kutsutsa boma, chirichonse kumangoti fwifwifwi. Mapayipi oti anayikidwa 1970s Someone wants to uplift ur status koma ziwindi thoooooo.
  Wht type of Emvitonmental Impact Assessment are u talking about.
  In Africa EIA is done just to please donors simple. Otherwise if EIA was really being practised we couldnt hv more unfilled pits risking our children along roads being constructed across the country. The socalled Mps only act when their stupid leaders tells them so to gain cheap political mailage.
  Ndiye mwati Chakwera, kunyumba kwake madzi ake muli chani???? kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk. Musovenge koma kumakana madzi ku lake malawi ati kuopa kuti Boma litchuka kkkkkk,

  1. In most countries you go, no matter how big or small the ocean or lake, simuzamva kuti akumwa madzi amu nyanja kapena mbwani! It’s only river water that’s is fresh to drink! Why? You asking! Because, rivers are always flowing fast, thereby taking the rubbish away with them which makes it easy to purify, unlike the lake and ocean which flows very slowly.

  2. Mr Ebrahim such countries can not take from their lakes or oceans because they have got salty water, Lake Malawi got fresh water and it has Shire river as an outlet that keeps the water of lake Malawi to keep on flowing,this will not be the first time for Malawi to use the water from Lake Malawi some areas in the lake shoe areas they already use the water from lake Malawi eg Nkhata-bay they use water from lake Malawi.

  3. Kodi osusa boma amapanga zoti anzawo alephere ndi cholinga choti apeze zoti aziwatozela anzawo uku ndikulephera chifukwa mavuto akagwa Malawi muno ndi atonse. Lero mukumwa madzi woyipa pomwe ndi inu nomwe mukukana zabwino

  4. I feel sorry indeed from my country,i feel ashamed too ,a malawian company being denied to be offered the contract but had it been is from uk hope opposition could hv allowed it to do the work.Amalawi sitinatope mkulemeresa anthu amaiko ena?

  5. Musamayambe Zina Et Zna Zkukanika Bwanj Osathana Kaye Ndi Magets Adazimawa Kt Ayake Kenako Muzganiza Zamadziwo Mukusowa Pobela Zna Ndalama?

   Idyan Kaye Zakuchimanga Zija Zkatha Ndye Muyambe Zabodzazo Kt Muzidzaso Bwno.

 52. Boma likufuna kukukokerani madzi from lake malawi kuti mumweko fresh water osati zigayigayi mukumwazi zakumalingunde zomwe amakala abibira, koma inu ati kudziwa kutsutsa boma, chirichonse kumangoti fwifwifwi. Mapayipi oti anayikidwa 1970s Someone wants to uplift ur status koma ziwindi thoooooo.
  Wht type of Emvitonmental Impact Assessment are u talking about.
  In Africa EIA is done just to please donors simple. Otherwise if EIA was really being practised we couldnt hv more unfilled pits risking our children along roads being constructed across the country. The socalled Mps only act when their stupid leaders tells them so to gain cheap political mailage.
  Ndiye mwati Chakwera, kunyumba kwake madzi ake muli chani???? kkkkkkkkkkkkkkkkkkkk. Musovenge koma kumakana madzi ku lake malawi ati kuopa kuti Boma litchuka kkkkkk,

  1. In most countries you go, no matter how big or small the ocean or lake, simuzamva kuti akumwa madzi amu nyanja kapena mbwani! It’s only river water that’s is fresh to drink! Why? You asking! Because, rivers are always flowing fast, thereby taking the rubbish away with them which makes it easy to purify, unlike the lake and ocean which flows very slowly.

  2. Mr Ebrahim such countries can not take from their lakes or oceans because they have got salty water, Lake Malawi got fresh water and it has Shire river as an outlet that keeps the water of lake Malawi to keep on flowing,this will not be the first time for Malawi to use the water from Lake Malawi some areas in the lake shoe areas they already use the water from lake Malawi eg Nkhata-bay they use water from lake Malawi.

  3. Kodi osusa boma amapanga zoti anzawo alephere ndi cholinga choti apeze zoti aziwatozela anzawo uku ndikulephera chifukwa mavuto akagwa Malawi muno ndi atonse. Lero mukumwa madzi woyipa pomwe ndi inu nomwe mukukana zabwino

  4. I feel sorry indeed from my country,i feel ashamed too ,a malawian company being denied to be offered the contract but had it been is from uk hope opposition could hv allowed it to do the work.Amalawi sitinatope mkulemeresa anthu amaiko ena?

  5. Musamayambe Zina Et Zna Zkukanika Bwanj Osathana Kaye Ndi Magets Adazimawa Kt Ayake Kenako Muzganiza Zamadziwo Mukusowa Pobela Zna Ndalama?

   Idyan Kaye Zakuchimanga Zija Zkatha Ndye Muyambe Zabodzazo Kt Muzidzaso Bwno.