M'modzi mwa omwe analowa chipani cha Malawi Congress (MCP) kuchoka ku chipani cha Democratic Progressive (DPP) a Ken Msonda ati mtsogoleri wa chipani cha DPP a Peter Mutharika sadzaima nawo pa masankho a chaka cha… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Yemwe anali wachiwiri kwa mtsogoleri wa chipani cha United Democratic Front (UDF) ku chigawo cha ku m'mawa a Hashim Banda ati masomphenya a chipani cha United Transformation Movement (UTM) anawakopa ndi chifukwa alowa chipanichi. Poyankhula… ...
In a calculated move to cut accommodation expenses, Mighty Mukuru Wanderers football club has inked a one-year partnership agreement with Golden Peacock Hotels. During the signing ceremony in Blantyre, Mighty Mukuru Wanderers' CEO, Panganeni Ndovi,… ...
Zadziwika kuti ophunzira ambiri a mu sukulu za ukachenjede chingerezi chikumawapeta ndipo ambiri sakwanitsa kufotokoza komanso kulemba m’chizungu chomveka bwino. Izi ndi malingana ndi otsatira kwa wachiwiri wa Chancellor ku sukulu ya ukachenjede ya University of… ...
Mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera wati sibwino kunamiza aMalawi kuti dziko likhonza kumangidwa popanda maziko ovuta komanso a misozi, ndipo kulankhula motha mawu otere ndi chifukwa choti omwe adali m'boma m'mbuyomu adaba ndipo palibe… ...
Mu masewelo a mpira wa miyendo okumbukira tsiku la mtsogoleri oyamba wa dziko lino a Ngwazi Dr Hastings Kamuzu Banda pakati pa Mighty Mukuru Wanderers ndi Silver Strikers pa Kamuzu stadium athela kukomera Wanderers. Mphunzitsi wa… ...
Mtsogoleri wakale wa dziko lino a Bakili Muluzi ati chisamaliro cha atsogoleri opuma chomwe boma limapereka chikufunika kuunikidwanso, ponena kuti pali zigwelu zambiri zofunika kukonza . Mtsogoleri wakaleyu wati, mwa chitsanzo, pakali pano amagwiritsa ntchito… ...