Be Forward Wanderers
Wanderers football club's captain Joseph Shakirah Kamwendo has started light training with his team after he sustained a harmstring injury on 29th october. According to Nomads' team doctor Samuel Matukuta, the captain is currently fine… ...
knife-blood
Apolisi m'boma la Machinga akwidzinga ndi kutsekera abambo atatu chifukwa chowaganizila kuti adachotsa moyo wa bambo wina wa zaka 60 pomukhapa ndi zikwanje. M'malingana ndi oyankhulira apolisi m'bomali Davie Sulumba, a polisi amangadi John Daudi… ...
Patience Namadingo
Atadzipereka yekha kusaka ndalama kuthandizira odwala cancer pogwiritsa ntchito luso lomwe namalenga adamupatsa, m'modzi mwa oyimba nyimbo za uzimu Petience Namadingo tsopano wamaliza zonse. Malingana ndi Namadingo iye wati tsopano wapseda zonse lero pa 24… ...