
Pamene anthu ena akugona ndi njala, ena pa mzere wa mafuta, ndipo mu zipatala mulibe mankhwala, boma latenga ndalama pafupifupi 5 biliyoni ya Malawi kupereka ku kampani ya ku Ghana kuti athane ndi a Bakili… ...