Ali kuti a Chakwera okonda kuyenda ndi kuyankhula ndi ife ana awo pano pamene nyanja yakalipa ndi ukali wa Covid-19? Akudabwa chomwecho a Malawi pamene chiwelengelo cha anthu opezeka ndi Covid-19 chikuchulukila. Adindo amene akutsogolela… ...
Malawi Hospitals
Ena akuti ikumveka ngati ya ma kadi ija a Malawi anaikana pa dzana mu ulamulilo wa Kongeresi. Ena akuti tisakambilane iyiyi pamene tikukanika kulimbana ndi katangale. Otakasika ena akutsindikanso kuti imeneyi ibwele ndithu, pasakhale munthu… ...
Bushiri Major 1
Kusiyana kwake sanapemphele, zitseko zandende sizinatseguke zokha, koma pamapeto pake moyo wake naye wasangalala. Amene amazitcha kuti mneneri ndipo ali ndi luso lodziwa za mtsogolo, Shepherd Bushiri, wathawa mu dziko la South Africa kumene amayankha… ...
The winter and spring months have been stressful for many. Several people have spent more time indoors this year than they wanted to. This meant a lot of time in front of the screen, working,… ...