Ras Chikomeni David Kadelele Chirwa yemwe amadziwika bwino ndi dzina loti Ras Chikomeni, ati ndi okonzeka kuyimanso ngati m’tsogoleri wa dziko lino pa zisankho za patatu mu 2025. A Chikomeni anali ndi chidwi choyima pa… ...