Lawaluma lamulo ndipo lawasiyila chilema chachikulu chokuti ngakhale a chipatala sangathe kukonza. Ndipo inu nonse okonda kuchitila nkhanza ena, bisalani patali chifukwa mawa mutha kukhala inu. Amayi atatu a ku Lilongwe amene anagwila mmayi mzawo… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Si zampira ayi. Apa zikungokhala ngati anthu ake ndi agalu achiwewe chenicheni oti akufunika kuswa ndi miyala. Anthu ena ochemelela timu ya mpira ya Bullets akuononga masewelo a mpira kamba ka khalidwe lawo lokonda ziwawa.… ...
…feared Malawi Police presence in a ‘foreign land’ Two districts are slated to announce their secession from mainland Malawi today, proponents for this move have confirmed. According to the Peoples Land Organisation (PLO) as led… ...
In the face of serious electricity problems, Malawi President Peter Mutharika has ambushed the Electricity Generation Company (Malawi) Limited (EGENCO) management in Blantyre. The President arrived at EGENCO offices at Umoyo House in Blantyre as… ...
Inu amene mukumadzuka usiku ndi kumakolezera moto pa nkhani zopopa magazi, samalani chifukwa Apolisi ayamba kunjata anthu a mkhalidwe onunkhawu. Mkulu wina wa mu boma la Zomba walamulidwa kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu chifukwa… ...
Salima South Legislator Uladi Mussa has insisted that he is still the party’s acting president and vice-president. The politician has claimed that the party has not told him that he was fired hence he is… ...
Amene amayesa kuti chipani cholamula cha DPP chatha ndi kufelatu basi kamba koti chathibulidwa ka ‘5 kwa 1’ ndi chipani chotsutsa cha Kongeresi, ati aganizenso kawiri. Malinga ndi mneneri wa boma a Nicholas Dausi amene… ...