Amunjata chifukwa chonama za ‘anamapopa’

167

Inu amene mukumadzuka usiku ndi kumakolezera moto pa nkhani zopopa magazi, samalani chifukwa Apolisi ayamba kunjata anthu a mkhalidwe onunkhawu.

Mkulu wina wa mu boma la Zomba walamulidwa kukakhala ku ndende kwa miyezi itatu chifukwa chonama kuti kuli anthu opopa magazi.

CourtMalinga ndi Apolisi, a Bambo Stanford Bamusi a zaka 49 anadzuka pakati pa usiku pa 16 Okotobala ndikuyamba kukuwa kuti mmudzi mwawo mwabwela opopa magazi.

Anthu adathawa m’nyumba mwawo ndi kukagona kutchire ati poopa kupopedwa magazi ngakhale kuti mderalo munalibe zimenezo.

Apolisi atamva izi, adamunjata mkuluyo ndi kumutsekela mu chitolokosi.

Atapita naye ku bwalo, iye anapezeka olakwa pa mlandu ofuna kudzetsa chisokonezo ndipo walamulidwa kukhala ku ndende kwa miyezi itatu.

Ngakhale mlandu otele munthu amaloledwa kupeleka chindapusa, bwalo linakana.

 

Share.

167 Comments

 1. Today people will say alot of things confusion n whatsoever wait when they come to ur house then u will say yah those people were nt lying that’s when u will learn trusting others why talking on sumthing that u knw it never knocked on ur door osakhala chete bwanji if u think ur super hero’s n clever pipo wait for ur turn muzatiuza

 2. God told a black man: ask me anything you want and I will give it to you, but I will give double to your neighbor. Then he started thinking. If I ask 10 billions he will give 20 billions to my neighbor, if I ask 100 billions, he will give him 200 billions. Then he asked God to remove one of his eyes. Ehhhhh Black man.

 3. Oooh tikamuona munthu oyipayo tisapulumuse ena?kuopa boma? Pamtumbo pawo abomawo achizimayi m’bomamo panyini pawo onse achizibambo mbolo zawo

 4. manso mwanu nonse mukuti opopa magazi kulibe.chipatala chadomasi kunabwera athu awili opopedwa koma sanawalabadile mpaka anapita kumalosa mkomwe anakawathilanso magazi.ziyakhulani zotumbwazo.awapopa abale anu mwava ndipo akanabwera kwanuko ndikupopa banjalonse musiye makani

 5. Nose amene mwaika ma comment apa ndikukuyamikani km ndi ine amene ndawatuma anyamatawo kuti agwire ka ntchito kamene ndiye musadabwe

 6. it’s true that there is blood succer and believe it but now it is going to ended by sinio tchief ngolongoliwa in thyolo.

 7. the police and local peopl in areas where remours are spreading on the issue should work hand in hand to findout the truth otherwise more innocent people will lose lives for nothing;our MP,do ur job professionaly

 8. Gyz enanu mlindimzimu koma?Nkhan yopasa chison ngat imeneyi mungamat ikukukwanan ena mpaka kukupasan mselu akupanga zmenezi mkwadziwa inuyo yet?Osanapanga coment yopusa apa ngat mlibe mawu just read and pas dont coment those no ncence here

 9. Asiyeni azitizunza choncho tionana 2019 wina adzagwapampando chifukwa cha nkhani imeneyi. Ifeyo amalawi tikudziwa anthuwa akudziwapokanthundithu bwanji asakubwerapoyerandikulongo solazamavuto amenewa anthutu sitikugona tikukhalangatianthuothawa nkhondo. Malawi watiipilakwambiri asatiopsyezeakuphqufuluwathu olankhula pazovuta zomwe zikutisautsa. Koma 2019 tidzagwila ntchito yotsitsapampandowina amalawi siopenga zikutinyansa ubwino wake ayambakalekuluza 2019 tizatsitsa Nyanimuntengo magazi athuwo awasiye.

 10. Kodi opapa magaziwa bwanji sakumapita kwa akuluakulu andale komanso achibale a apolisi ndi asilikali nkumakaazunza mesa akufuna evidence pamenepo mpomwe adadaipeza mwachangu osati kumangoazunza amphawi coz zayamba kutembenuka sopano.. instead of helping the victims..u r now arresting them..why??

 11. good idea police arrest them, kudzolowela ndiwawa basi, why keeping govmnt restless since 1994, bakili mbuli mbuli, bingu arogant, joyce cashgater, pitala nde chilichonse chamugwela, Pano Tayamba Kujiya Ya Chakwela 2019 yinyamuke naye tidzamusautse kkk. nyumba yikupsa, usi wudzioneka.

 12. Kodi ndizoona kuti mpaka pano umboni siunapezeke? Ngati zili nchochi nkofunika kuti apolisi atengepo action pa hearsay imeneyi, mbiri ya dziko isamangoipa pa zinthu zopanda umboni.

 13. hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email drodudu36@gmail.coml , pardon me i offend you with this post, but i must share this good news

 14. If it is not true how come that it was in mulanje now Blantyre that means anthuwa ndi amisala? Ok president amakatani ku mulanje amakayendera anthu okhuzidwa

 15. ineso zimenezi zandikwana ndikucita kuva nazo seru ndi khani zopanda umboni ndindani aganene zowonadi pazimenezi? gayz we are west time. kumalimbana ndi zazi kuleka kupanga zatsongolo lanu

 16. hope the blood suckers will kip on doing it until someone with his big white shirt and black jacket out side will have a proof as well chifukwa mbiri sipita popanda nkhani mwina poti ndine mwana mwina obadwa kalewo amadziwa kuti pali malo ena otuluka utsi kma popanda moto

 17. Nbanjatu kupereka ufulu kumankhala kusalikonda banjalo pali ndiufulu wake tawonani chipani chimozi sitinkavutika ngati mmene tikuvutikiramu taonani tingophana chuma chalowa pansi komanso ufulu omwe uja lelo siuli bwino kodi nziko mwanthu tizinkhala mwankhumakhuma? Simumati munthu utchula nzake kuti ndimfiti amangidwe? Tawonani lelo siufiti uwu eeeeee if do you creetside say nothing and be nothing malawian its over now

 18. Kodi ndi angati omwe apopedwa magazi so far? Boma lakhala likufuna maumboni kwa anthu omwe apopedwa magazi koma mpaka pano sakupezeka, ndizoona zimenezo? Anthu inu musamati mukamachokera kokatamba usiku nkumanamiza kuti anthu akumapopa magazi, pelekani umboni kwa munthu mmodzi amene wapopedwa magazi. Mukuyipitsa mbiri ya Malawi yabwino yomwe adayisiya che Kamuzu chifukwa chosapota zipani zopanda ntchito. Anthuwo azimangidwa ndiponso azimenyedwa asiye zachibwana zomwe akupangazo. Ngati sitidziwa Democracy tiyenera kwafunsa anzathu omwe adayiyamba kale mmaiko ena. Ife tikwasapota apolisiwo agwire ntchito mosaopa ayi akupanga zamasewera ndi boma salidziwa.@#continue Mr president.

 19. muzivutilanji tiyeni timusilemulungu mkhondo imenei ndipo palibechomukanika mulungu ndipo kwaonse ochita zimenezi mulungu awa khululukile palibe chimene akudziwa

 20. Munathesa Vakabu Lero Amalawi Sakugona Akuzuzika Kamba Ka Anamapopa Nde Sizowona Kut Apolice Muzingomanga Anthu POngomva Akukamba Zamkhaniy Ndibwino Kumanga Munthu Mutangwila Akupopa Umenewo Uthakukhala Umbonid Wenwen .

 21. Anthu mukumagona osasamba,kudya nsima mitanda 5,usiku mukuchezeletsa mkazi,mpaka 6am,mukatero tea mukumamwa 10am,ndye ndi dzuwa limeneli mukumafooka mukatelo mukuti akupopani magazi hahahaha..

 22. Kodi a police mwauyiwala ufulu oyankhula za kukhosi?nanga.mukamanga anthuwa ufulu wawo uli kuti?nthawi ya chipani chimozi inali bwino zovuta zinalipo koma zachisawawa kunabe,lero muti democracy koma zingofanana nevertheless ife ngati nzika tizayankhulabe,koma tisanatelo tilemekeze lamulo komanso kuyankhula zinthu zomwe zili ndi umboni

 23. machende amakolo awo omangao abwere azamange ine.Iwo akuona ngat anthu angakhale openga malawi yonse kumat kuliopopa magazi? Zikoli peter waligulitsa mbuz yamunthu.Abwere kuno ku kwa gaisi azandimange.Machende ambuzi

 24. Anthu openga munakhala bwanji mwasinthaso mesa ndinu nomwe mamuzikokomeza lero mukut zongopeka mwaona zikusowekera umbon kumangofalisa nkhani koma yopanda umboni anthu openga

 25. Chilungamo chikusowa pa nkhani iyi koma chomwe mungadziwe mulungu azakantha omse akuchita za ku mm,dima ambuye akukhululukileni pomanga anthu kukana chilungamo munthu sanganame pa nkhani iyi dziko ndi anthu ake

 26. Amangidwe anthu otele,ngati zalowa ndale kuti atchuke,pofuna kuipitsa mbiri yaena!! Azione.Palibe yemwe umboni oti zikuchitikadi,ngati alinawo umboni aonetse a Police ndikupitiliza kuyankhula zokhuza opopa magazi.

  • iwe siyakhaniyo wamva athu akupopedwa kuzela m’masenga moti akapita kuchipatala akumawawuza kuti akudwala malungo izi sizoti ungaziwone ndi maso pimwe akumwela magaziwo there using magic satanic moti muthu akafika ofowoka kuchipatala adotolo akumati ndimalungo akulu

  • Mercy & Levison Mopanda Kukuchoselani ulemu Wanu Ziwani Izi : { A} Zoti Kuli Mablood Suckers Ndi Zoona . Chomwe Chikuvuta Ndi Choti Amene Akuletsa Ndi Anthu Oti Mwina Sadazione . Ine Personally Have Seen A Victim At Laiti 2 Village In T/ A Bvumbwe’s Area Near Bindula CCAP CHURCH. It took Place On 17/10/2017 & Another Ordeal Happened On 19/10/2017 in the same village . The Victims In These INcidences Are Females. The Security Agencies Are Aware . { B } Am Of The Opinion That These Are Politically Motivated Attacks By Some Gurus Who Are Serpently Crafting The Exit Door For The Current Regime. They have opted for divide and rule means. They Know Attacking The Populace Will Erode The Confidence In The Regime Thereby Creating An Appitite For Regime Change Come 2019 . You know , who doesn’t want to live in a secure society. hahahaha. Am very sure that you have grasped something relatively tangible. May The DPP wake up and stop being myopic.

 27. hello friends my name is Edith Ngeny I never knew there is now cure for HIV until i got cured from the virus by one herbal doc called Dr ABUMEN, I was positive for 7 good years,taking ARVS until one lady told me of how he cured his sister from the virus, I contacted the doctor through his whatsapp line +2347085071418 and started taking his herbal medicine and exactly after some days i went for a test and i was diagnosed to be negative.Series of other tests proves i am still negative of the virus today. You can contact him now if you are affected with this virus because when u keep silent the virus will eat you up, You can also email him for any kind of help via email (doctorabumen@gmail.com) or whatsapp him on +2347085071418