Breaking: Mutharika makes surprise visit to Egenco


Malawi President
Malawi President
Mutharika visits Escom

In the face of serious electricity problems,  Malawi President Peter Mutharika has ambushed the Electricity Generation Company (Malawi) Limited (EGENCO) management in Blantyre.

The President arrived at EGENCO offices at Umoyo House in Blantyre as time was clocking 10:20.

As this is a developing news, Malawi24 will keep you up to date.

243 thoughts on “Breaking: Mutharika makes surprise visit to Egenco

  1. Surprising who? Vendors or passersby. According to the information I have, the management was aware and this is evidenced by the general cleaning that was carried out a day before this so called surprise visit.

  2. 1966 tinalandila ufulu wodzilamulila koma sitili paufulu wodzilamulia pachuma,tidziwauza achinyamatawa kalekathu,a Bingu ankafuna kuti tikhalepaufulu wadzachuma,tiyeni tigwilane mania,titukule dzikolathu,

  3. Kkkkkkk vuto la udindo wosauvutikla nd limenel u don’t know how to do important things in their right time.Nanga te mwaxwa lero kt kul power crisis???? Azanu akutulukilan simuothera2 apa Man. wa nyanya ur stupidity is spoiling each and every Malawian ukulitenga dziko ngat la achimwene awo ambuye Wako ndithu.

  4. After visiting escom, mr president, the blackout has increase spontenously with 6hrs of blackout per 30 mins of light in 24hrs. Thanx mr for improving blackout not the light.

  5. Politics aside tiyeni tiganize izi: Tikamavota sititanthauza kuti boma lizitipatsa thandizo khomo ndi khoma ai koma lizipanga zokomera mzika zake…anthu azitha kupanga timabizines mkumathandiza mabanja so.
    Tiyeni tione anthu ngati awa: wa barber shop, welder, wa Chigayo, was saloon komanso wogulitsa chicken parts. Mukuti anthu amenewa zikuwathera bwanji??
    OK pitani Ku makampani anthu akuchotsedwa coz sakupanga phindu lokwanira coz magetsi kulibe aku gwiritsa ntchito ma generator omwe safikira ntchito zao xonse…..
    OK China mukuyembekezera kuti wina angachoke kunja kuzayambitsa kampani yake mu dziko LA m’dima?

  6. Hahaha dzidzimuka akudabwa apa yavutz ndi 5 kwa 1 zochedwa 2 late ife pano sitingaiwale olo magetsi atayamba kuyaka wl stl remember kuti timakhala opanda magetsi 20hrs a dy

  7. Not tooo late as such still more time..APM……let us make conclusions…if. Koma ife amalawi ndife atulo timaona zalelo kusiya zapamawa……let’s think of bingu…..remember….one mistake will make us suffer..for so long

  8. Umapangitsa Ndi Umbuli Zoona Ukudziwilathu Kt Dziko Lanthu Ndilaling’ono Iwe Ndikubwela Kufuna Kudzalamulira Ukt Ndine Profesor Ndiye Watha U Profesor Wako Dziko Linamkwanila Bakili Muluz Ndi Joyce Banda Zinthu Zimayenda Kozan Magets Ngat Aprofesor Azanu Ma Doctor Amayendetsa Uyu No Sense Kma Wamkulu Ndiwe Uchititsa Manyaz Sitikuuona Umuna Wako Mutha Kuipa Mtundu Wanu Mkuzuza Amalawi Ambiri Zandiwawa

  9. I 100% believe that that is just a public stunt.His surprise show in the board meeting won’t all of a sudden change the deep rooted problems rocking the power supplying company.That was just a desperate attempt to regain long gone public confidence

  10. its avery welcome development his visit can change things! These Electricity people have failed to perform “qualified but not competent ” panopa azimayi ali khumakhuma muzigayo kuti mwina ana akadye! Wina achotsedwe ntchito kayekoma.

  11. Zikhoza kutheka kuti mwina magets anazima ku State house and so a President zawakhuza. I certainly hope that this surprise will lead to a more efficient and sustainable outcome

  12. Nkhaniyi siyachisankho ndikhani yadziko zikachitika atsogolereli amaiko kuendera muzinchito kumamva kuti vuto lenileni ndichani mcp cn win bt it will never rule malawi again thank u H.E kumenekoso amcp aliko motiso nthawi yanchito chifukwa chofuna chipani chawo chilamure amapita kumbayani nthawi yanchito kuchibuku every day cholinga akuoneni kulepera olo muesese sadzayamika malawi ndimamudziwa wake ndimwano nsanje kaduka

  13. Zamanyazi Nthawi Ya By-election Magetsi Samathima Koma Atalengeza Zotsatira Eishi Anthu Aku Nchalo Ndi Nsanje Tikuvutika Magetsi Akumangothimathima.Tidalakwanji Ife Anthu Aku Lower Shire.

  14. When a white man creates a phone and you video chat with your brother you call it technology but when your Grandmother in the village use a mirror to see you in the city you call it witchcraft. It’s about tym we value our africain products.

  15. This Time Yot Amalaw Tseguke Mutu Becoz Aona Zot Ma vote Ayandkila Ayamba Kut Kopa, The Moments He Win Azayambaso Kutnyoza Chenjelan Azanga

  16. zaziiiiiiiii ndimawona azIti agula machine ena zimenezi ziyathandiza chani a malawi kapena ukufuna kutimphimba m’maso ndiye walemba m’madzi phwamba Malawi adachangamuka sizakale zija plz try another plan

  17. Katangale pena poliponse dziko liyenda bwaaaa???yamba Kaye kumanga nduna 7 zija ndi chapo komaso musiye mwano mudziwe kuti mabwana anu ndife, anthu tikuvutika umphawi mamidzi osaneneka, misonkho penapaliponse

  18. Loooooool is too let ……… even the president why is facing them bt long-time we hv this problem in Malawi ……… zinazi zimadidabwisa bwanji a president ogona tulo

  19. DPP tikangoyikaso pitala kuti akapikisane ndi chakwela ha ha mwayenda omweo akuchepa pitala MCP MMM sikubwela bwino

  20. Mai Joyce banda munayesesa petrol amavuta magisi amavutaso koma 3 month zithu zinali BWINO koma pano DPP yalowaso 3years pano MMM kaya

  21. Ine kumuzi pheee waka chigayo cha diesel,kuyasa kandulu ,mazi pamjigo,kuphika nkhuni,radio tigerhead battery ‘foni charge solar mukutipo bwaaaah?

  22. I applause the president,because ESCOM &Ministry of Energy and Mining to be removed.Some bosses at ESCOM they do what they want because like yesterday electricity were on 3:00 pm and it was off 12:00 pm and has been on 7:00 am only line of lilongwe here in Kasungu while nkhotakota line is off till now.ESCOM officials they steal from us,when we ask them they every day.what kind of life is this?Ministry of trade and industry too is killing us while people strugles in their pockets everyday to survive.things are expensive on the market.

  23. Electricity issue has reached a point of NATIONAL DISASTER, if he was an active president he would have just declared so before leaving those offices. The citizens are now paying dearly because of this

  24. mcp resurta
    1994-fail
    1999-fail
    2004-fail
    2009-fail
    2014-fail
    2019-fail

    kkkkk mizimu yachina gadama idaķwiila komanso aņthu aja amaponya mudziwe lang’ona komanso ayufi kugwilila azimayi ndikuba ziweto. .mulungu adachitembelera chipani chimenechi sichidzalowaso m’boma

  25. poti aliyense ali nkuganiza kwake koma ine ndikuti, wachita bwino kungowatulukila, wazionela yekha kufooka kwao, waonanso kuti akutipasa umphawi omakhala nthawi zambili opanda magesi kugona muum’dima anthu ambili tinazolowela magesi ukazizimuka kuyang’ana munthu wa mai umati shaaaaa, kooma ndiwe wemwe iye alintulotu kenako umamugundagunda kuti mmmmm miisa ziyendepo aaaa upeza wachinya chigoli ukalimbalimba mwinanso zigoli ziiwiili koma kusapeze kwa magesi aaaaaa ambwiye ukangoti phiiiiiiii, ndi phiiiiii basi ungozizimuka kwacha pomazati mwina wansembe naye afune umaona nthawi yatha ndiye presdent wachita bwino sanalakwise wachita mu nthawi yomwe zafika poipa kukhala mu m’dima ndiukaidi omwe

  26. Vote of thanks to mcp. The guy is waking up now, though too late. Solution: Return all the moneys Dpp has been collecting from escom and thereafter beg heavenly Father to open the sky water gates. Just an ambush is not enough.

  27. Egenco offices are in Chayamba Building while Escom offices are in Umoyo House opposite FDH Bank. The picture above depicts he went to Escom offices in Umoyo House. Of course the story is VERY TRUE and it has just happened a couple of hours ago.

  28. Ine amenewa amandichititsa mselu mxii magetsi kuzimitsa sitikana but not 12 hrs everyday amakhala akukonza chaniii all this time solution sanapeze, mxii

  29. Ameneyo Ndimunthu Wokuba Mmalo Mot Akanapita Mozizimusa Ku Mkula Kapena Kutedzani Falls, Akupita Ku Maofesi Kut Akabe, Ndiye Akabako Chani Pot Anzake Abako Kale, Chindele Chakufikapo

  30. Ndakhala ndikunena ine mu nthawi ya joyce banda magetsi dangosintha nkuyamba kuyaka bwinolomwe ngakhale water level idali yotsika an indication kuti it was sarbortage and it is sarbotage by some clan which has dominated management ranks of escom. Achoke anthu oterowo achoke

  31. last week i felt like was in america cause magetsi anayaka one week. pamene ma vote anangoti atha magetsi so anayamba ku zima. this simply means ndizandale. I don’t care what he is all up to!!! I will never live in malawi in my future days. ndizakakhala kumene magetsi sazima, in fact aliyense amene amagwiritsa magetsi ntchito have got plan ngati yangayi. muzatsara nokha!!! muziza thimitsa bwino#.Escom ndi andale.

    1. Kkkkkkkkk Ronald go back to school, bolanso anakayendera power stations nanga Ku office?, after all inviting board members to state House is cheaper comparing to the president motorcade.

  32. Do you believe HIV is now cureable, with the help of Dr. Tiam I was cure of after 9 years staying positive and using ARVS. His herbal medicine is very strong and reliable. You can call or WhatsApp him for all kind of deadly and undeadly diseases like, weak Erection, prostrate cancer, kidney problem, penis growth and enlargement, sexual problem, fibroid etc: +2348037284837

  33. A horse is failing in three years but the cow pulled the same log in few months. … flex your muscles before the log falls on you

    1. Rubbish and niussance talking! Is this South Africa! You rely electrify from other countries! If they want to punish you ,its within seconds! Go to Nigeria Zimbabwe the scenario is the same but you are boosting yet you don’t generate your own power!

    2. Panyopako unalephera kupeza ntchito kuno pano usoka nsapato galu iwe! Kumeneko ndikwanu? Mkamwa monunkhamo. Tiona sulibe passport!

    1. If I were a potential investor and I had an option of where to do my business I wouldn’t bring it to Malawi with this kind of energy crisis

  34. Too late! Mwabetsa kale ma vote and akulangani a Egenco achita dala! If asked , they will answer you with their Technical answers to save their jobs! Last month we had lights from Saturday up to Tuesday without blackout, where did they source this power! These blackouts are political masterminded!

    1. @Kazembe Alisen James! Seems u are lost here! Should now generation suffer at the expense of others? All we need is instant solution not because Malawi is for ever! That’s misconception!

    2. small mind! Why should I rewrite! It shows you are mad! Are you living in the future generation? Do you know what technology will be used by then?

    3. Rewrite what! You should re write! We are suffering today, should we talk of the future? Technology is changing all the time,do you expect that in the future it will be the same technology! It shows you are myopic!

    4. Wamakani ndiinu akulu ! Inu sinukuvutika monga! Same as kusunga Ndalama ku bank inu mugona ndi njala,nyumba mulibe,ana akulephera school kusowa fees! Work of small mind!

    5. Zomwe mukukambirana apazi zikuonesa immaturity kodi basi mumaona ngat mavuto anu azawasove ndi a boma? Bwanji osagula solar ngat mukufuna magesi .tilimbikire ntchito kut ana athu asazavutike ngat ife lero. Kuzolowera za ulele basi aaaaaa ndanyasidwatu. Be mature

    6. Akulu that’s childish! If I have the solar do you mean the rest who can’t afford will benefit this? Don’t be selfish if you are rich ,YOU ARE NOT RICH! There people with money and on nice jobs, but they are concerned with those who can’t afford! I can see you you don’t even have anything! The money government spend its our own money not from your pocket! So stop nuisance comments and love everyone as you love yourself.

    7. That’s bushit to be concerned is it the way of solving the problems of people? My brother don’t talk shit otherwise you gonna get hit. Do you know me? If you do such things to others stop it. Who are you? If you keep on talking bushit am Going To scrutinise you. You think am afraid of you? Who authorised you to reply my comment? Are you wiser than all those people? Be wise for you to be respected. Tizapondanapo pano kkkkk usamale aise wamva .kkkkk mwaona zosatira za magesi kkkkk tikuyambana

  35. Is he serious? This guy is a crook. All these is bcz of being embarrassed with by elections. Pple have been talking since day 1 that he should not depend on informations from his cronies. He must go out and assess himself what is happening

  36. Aaaah Kusonyeza Kut Uthenga Wawafika Kumene Kut Magesi Akumavuta? Paja Kwawo Samazima Eti,mchifukwa Chake Samaziwa,ndikutha Kuona Kut Aidabwa Abwana Dausi Amawanamiza Pano Aona Kut Azingoyenda Okha! Nde Ayaketu Mukamachoka Kumeneko Bwana Chifukwa Ife Kuno Tinaiwala Zamagesi,ana Afika Pomapanga Mzende Waya Wa Escom Sakumuopaso Iai.

  37. thats good mr president for that surprise visit anenedi choona cheni cheni amenewo za genset zija ziripati ofunika ena athotholedweko

  38. Zija anthu akhala akunena zakuti akuluwa amangodzitsekela ku sanjika lero adzidzimuka kutulo tofa nato atawona 5_1 .Amakhala ngati sali mu dziko momwemo azigwila sanati nthawi yawachepela kwangotsala chaka ndi miyezi palibe chomwe angasinthe anali ntulo ku state house

  39. Monsemuja samadziwa kuti magetsi akuvuta? Zinthu zoti mzimayi anakonza in one month period, kubwera azibambo kuononga ononga ndukanikanso kukonza mpaka zaka zitatu. NDE uzimbambo ulipati?

    1. Aaaa nanu inu nkhalani serious amai mmene amatenga boma kunali mabvuto amafuta mmene imatha 2months mafuta anayamba kupedzeka komanso magetsi samazimazima ngati mmene akupangira pano Amathuwo nawo kumbali yawo anayrtsesa ndithu

    2. nangapoti mayiwo amathandizidwa ndi mayiko akunja ndolo ndi peter muthalika akuyendesa dziko popanda mayiko athandizila burget yathu ya dziko lamalawi kumayamika pena

    3. kuteloko muthu akakhala osowa zochita zosatilazake amakhalila kunyoza athu oti sakuwaziwa kuti amapanga zotani pa umoyo wawo!!!!!!! mulindi mzelu ndinu mukulibana ndi politics ife opanda mzelu tikulibana ndi kusaka ma RANDS PA RSA kkkkkk a john ndi

  40. If He just called the EGENCO TO his office for the sake of making IT EASY otherwise him just steping out of the door an allowance is out aswell So instead of finding solutions his just bizy thinking about how much his gona get for tht journey

  41. Joyce Banda was able to solve power outage just in a month after commissioning kapichira project, what difficulties is this current government facing that makes it unable to do the same?

  42. the recent by election teaches him a lesson that his minions are blinding him that things are ok on the ground.
    if he now wakes from slumber and pay attention to what Malawians need he will gain political mirage in 2019.

    1. This electricity issue! Nothing to mix health sector! Issue on the ground is massive blackouts which Queen’s is also facing like any other hospital!

    2. Iwe Jeofrey ukuyankhula ngati queens udamanga ndi ndalama zamthumba mwakotu..zithe zimenezo olembedwaso chosecho apo bii ndiwe mmodzi mwaiwo

    3. Jeoffrey Mbeyau you have missed my point just go to queens and see how conjested and dirty the place is. If her make such a visit it will be a wake up call to all departments. Doctors are working in very pathetic environment

Comments are closed.

Discover more from Malawi 24

Subscribe now to keep reading and get access to the full archive.

Continue reading