
Moto wawotcha ofesi yowulutsilako mawu ndi zinthunzi ya kanema wa Luntha ku Lilongwe. Malingana ndi uthenga omwe akulu akulu ku wailesiyi atulutsa ati padakali pano sakudziwa chomwe chinayambitsa motowu. Iwo apitiliza kunena kuti motowu wawononga… ...