Kwa nthawi yoyamba tsopano kuchokera mchaka cha 2017, banki yayikulu pa dziko lonse ya World Bank yalengeza kuti ipeleka thandizo loti lithandizile mundondomeko yazachuma mdziko lino. Ndipo padakali pano yapereka ndalama zokwana 137 miliyoni dollars… ...
Articles By Ben Bongololo
Zina ukamva kamba anga mwala, zina zikamachitika nkumati kodi ndiku Malawi komkuno? Inu anthu am'mudzi mwa Chimombo mdera la mfumu yayikulu Kachere m'boma la Dedza lero pa 12 December ali kukamwa yasa atapha njoka 301… ...
A Bon Kalindo akhala akusungidwabe mchitokosi cha apolisi uku akudikira chigamulo kuchokera kwa woweruza milandu a Muhammad Maxwell Chande lachisanu likudzali pa 15 December. A Kalindo anawanjata sabata latha m'boma la Zomba powaganizira kuti iwo… ...
A polisi mu mzinda wa Lilongwe ku Area 3, anjata a Jonathan Nkhosa yemwe ndi mphunzitsi wa kupulayimale wa zaka 51 zakubadwa, kamba kobera anthu powanamiza kuti ndi wapolisi. A Nkhosa akhala akuchita bodza kwa… ...
Akaidi pa ndende ya Kasungu lero pa 5 December anali pa mwambo okumbukira ufulu wa chibadwidwe pa mutu woti "Ulemu, Ufulu ndi Chilungamo kwa Onse." Ndipo ngati njira imodzi yofalitsira uthengawu, iwo anagwiritsa ntchito maluso… ...
Sukulu ya ukachenjede ya Kamuzu University of Health Sciences yalengeza kukwera kwa sukulu fizi kuchoka pa K400,000 komanso K550,000 kufika pa K1 million pa chaka. Malingana ndi chikalata chomwe asayinira ndi a Chikondano Mussa yemwe… ...
Kutsatira mavuto omwe alipo kamba ka namondwe wa Freddy yemwe adaononga mbewu ndikuyika a Malawi ochuluka munjala yadzaoneni, tsopano boma layamba kugawa chimanga komanso ndalama m’madera omwe adakhudzidwa. Ntchito yopereka thandizoli yayambira mu mzinda wa… ...